Numeri 3:27 - Buku Lopatulika27 Banja la Aamuramu, ndi banja la Aizihara, ndi banja la Ahebroni, ndi banja la Auziyele ndiwo a Kohati; ndiwo mabanja a Akohati. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Banja la Aamuramu, ndi banja la Aizihara, ndi banja la Ahebroni, ndi banja la Auziyele ndiwo a Kohati; ndiwo mabanja a Akohati. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Aamuramu, Aizari, Ahebroni ndi Auziyele, anali mabanja otuluka mwa Kohati. Ameneŵa ndiwo amene anali mabanja a Akohati. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Kwa Kohati kunali mabanja a Amramu, Aizihara, Ahebroni ndi Auzieli. Awa ndiye anali mabanja a Akohati. Onani mutuwo |