Numeri 3:26 - Buku Lopatulika26 ndi nsalu zotchinga za kubwalo, ndi nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo, lokhala ku chihema, ndi ku guwa la nsembe pozungulira, ndi zingwe zake za ku ntchito zake zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 ndi nsalu zotchinga za kubwalo, ndi nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo, lokhala ku Kachisi, ndi ku guwa la nsembe pozungulira, ndi zingwe zake za ku ntchito zake zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 nsalu zochingira bwalo, nsalu zochingira khomo la bwalo lozungulira chihema cha Mulungu ndi guwa lansembe, ndiponso zingwe zake. Ankagwira ntchito zonse zokhudza zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 ndi makatani wotchinga bwalo, katani ya pa chipata cholowera ku bwalo lozungulira Chihema ndi guwa lansembe, zingwe ndi zonse zokhudzana ndi ntchito yawo. Onani mutuwo |