Numeri 29:9 - Buku Lopatulika9 ndi nsembe yao ya ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta, atatu a magawo khumi akhale a ng'ombe, awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo imodziyo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 ndi nsembe yao ya ufa wosalala wosanganiza ndi mafuta, atatu a magawo khumi akhale a efa wa ng'ombe, awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo imodziyo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndipo mupereke chopereka cha chakudya chosakaniza ndi mafuta, wa makilogaramu atatu pa ng'ombe yamphongoyo, wa makilogaramu aŵiri pa nkhosa yamphongoyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pa ngʼombe yayimuna iliyonse, muzikonza chopereka cha chakudya cha makilogalamu atatu a ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta; pa nkhosa yayimuna iliyonse makilogalamu awiri; Onani mutuwo |