Numeri 29:8 - Buku Lopatulika8 koma mubwere nayo nsembe yopsereza kwa Yehova, ya fungo lokoma; ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, anaankhosa asanu ndi awiri a chaka chimodzi; akhale kwa inu opanda chilema; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 koma mubwere nayo nsembe yopsereza kwa Yehova, ya fungo lokoma; ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, anaankhosa asanu ndi awiri a chaka chimodzi; akhale kwa inu opanda chilema; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 koma mupereke kwa Chauta nsembe yopsereza, yotulutsa fungo lokoma. Ikhale ya mwanawang'ombe mmodzi wamphongo, nkhosa imodzi yamphongo, ndi anaankhosa asanu ndi aŵiri amphongo a chaka chimodzi. Musankhule nyama zopanda chilema. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Muzipereka kwa Yehova nsembe yopsereza, yotulutsa fungo lokoma lokondweretsa Yehovayo; ngʼombe yayimuna imodzi, nkhosa yayimuna imodzi ndi ana ankhosa asanu ndi awiri a chaka chimodzi. Zimenezi zizikhala zopanda chilema. Onani mutuwo |