Numeri 29:10 - Buku Lopatulika10 limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 ndiponso wa kilogaramu limodzi pa mwanawankhosa aliyense. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 kilogalamu imodzi pa mwana wankhosa aliyense mwa asanu ndi awiriwo. Onani mutuwo |