Numeri 29:5 - Buku Lopatulika5 ndi tonde mmodzi wa nsembe yauchimo, yakutetezera inu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndi tonde mmodzi wa nsembe yauchimo, yakutetezera inu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Muperekenso tonde mmodzi kuti akhale nsembe yochitira mwambo wopepesera machimo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Muziperekanso mbuzi yayimuna kuti izikhala nsembe yopepesera machimo anu. Onani mutuwo |