Numeri 29:4 - Buku Lopatulika4 ndi limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndi limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 ndiponso wa kilogaramu limodzi pa mwanawankhosa aliyense. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pa mwana wankhosa aliyense mwa asanu ndi awiri aja muzipereka kilogalamu imodzi. Onani mutuwo |