Numeri 29:3 - Buku Lopatulika3 ndi nsembe yao yaufa, ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta, atatu a magawo khumi akhale a ng'ombeyo, awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndi nsembe yao yaufa, ufa wosalala wosanganiza ndi mafuta, atatu a magawo khumi akhale a efa wa ng'ombeyo, awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Muperekenso chopereka cha chakudya chosakaniza ndi mafuta, wa makilogaramu atatu pa ng'ombe yamphongo iliyonse, wa makilogaramu aŵiri pa nkhosa yamphongoyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pa ngʼombe yayimuna iliyonse, muzipereka chopereka cha chakudya cha makilogalamu atatu a ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta. Pa nkhosa yayimuna iliyonse muzipereka makilogalamu awiri. Onani mutuwo |