Numeri 29:2 - Buku Lopatulika2 Pamenepo muzipereka nsembe yopsereza ya fungo lokoma kwa Yehova; ng'ombe imodzi yamphongo, nkhosa yamphongo imodzi, anaankhosa asanu ndi awiri a chaka chimodzi opanda chilema; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pamenepo muzipereka nsembe yopsereza ya fungo lokoma kwa Yehova; ng'ombe imodzi yamphongo, nkhosa yamphongo imodzi, anaankhosa asanu ndi awiri a chaka chimodzi opanda chilema; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndipo mupereke nsembe yopsereza, yotulutsa fungo lokomera Chauta. Ikhale ya mwanawang'ombe mmodzi wamphongo, nkhosa imodzi yamphongo, anaankhosa asanu ndi aŵiri amphongo a chaka chimodzi, opanda chilema. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Muzipereka mwana wangʼombe wamwamuna mmodzi, nkhosa yayimuna imodzi ndi ana ankhosa asanu ndi awiri a chaka chimodzi wopanda chilema monga nsembe zopsereza, fungo lokoma kwa Yehova. Onani mutuwo |