Numeri 29:23 - Buku Lopatulika23 Ndi tsiku lachinai ng'ombe khumi, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai, a chaka chimodzi, opanda chilema; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndi tsiku lachinai ng'ombe khumi, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai, a chaka chimodzi, opanda chilema; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 “Pa tsiku lachinai mupereke ng'ombe khumi zamphongo, nkhosa ziŵiri zamphongo, anaankhosa amphongo khumi ndi anai a chaka chimodzi opanda chilema, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 “ ‘Pa tsiku lachinayi muzipereka ngʼombe zazimuna khumi, nkhosa zazimuna ziwiri ndi ana ankhosa aamuna khumi ndi anayi a chaka chimodzi, zonse zopanda chilema. Onani mutuwo |