Numeri 29:24 - Buku Lopatulika24 nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa, monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa, monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 pamodzi ndi zopereka zake zachakudya ndi za chakumwa pa ng'ombe zija, pa nkhosa zija, ndi pa anaankhosa aja, molingana ndi chiŵerengero cha nyamazo ndi potsata malangizo ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Pamodzi ndi ngʼombe zazimuna, nkhosa zazimuna ndi ana ankhosa, muzipereka chopereka cha chakudya ndi chakumwa molingana ndi chiwerengero cha nyamazo. Onani mutuwo |