Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 29:22 - Buku Lopatulika

22 ndi tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe yake yothira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 ndi tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe yake yothira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Muperekenso tonde mmodzi kuti akhale yopepesera machimo, kuwonjezera pa nsembe zopsereza za tsiku zija, pamodzi ndi zopereka zachakudya ndi za chakumwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Muziperekanso mbuzi imodzi yayimuna ya nsembe yopepesera machimo, powonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku pamodzi ndi chopereka chake cha chakudya ndi chakumwa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 29:22
6 Mawu Ofanana  

Zidzachuluka zisoni zao za iwo otsata Mulungu wina. Sindidzathira nsembe zao zamwazi, ndipo sindidzatchula maina ao pakamwa panga.


Mudzimangire chiguduli m'chuuno mwanu, nimulire, ansembe inu; bumani otumikira kuguwa la nsembe inu; lowani, gonani usiku wonse m'chiguduli, inu otumikira Mulungu wanga; pakuti nsembe yaufa ndi nsembe yothira zaletsedwera nyumba ya Mulungu wanu.


Nsembe yaufa ndi nsembe yothira zalekeka kunyumba ya Yehova; ansembe, atumiki a Yehova, achita maliro.


Kaya, kapena adzabwerera, nadzalekerera, ndi kusiya mdalitso pambuyo pake, ndiwo nsembe yaufa ndi nsembe yothira ya Yehova Mulungu wanu.


ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake;


Ndi tsiku lachinai ng'ombe khumi, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai, a chaka chimodzi, opanda chilema;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa