Numeri 29:19 - Buku Lopatulika19 ndi tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 ndi tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Muperekenso tonde mmodzi kuti akhale nsembe yopepesera machimo, kuwonjezera pa nsembe zopsereza za tsiku ndi tsiku zija, pamodzi ndi zopereka za chakudya ndi za zakumwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Muziperekanso mbuzi imodzi yayimuna ya nsembe yopepesera machimo powonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku pamodzi ndi chopereka chake cha chakudya ndi chakumwa. Onani mutuwo |