Numeri 29:18 - Buku Lopatulika18 ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira, za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa, monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira, za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa, monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 pamodzi ndi chopereka cha chakudya ndi cha chakumwa pa ng'ombe zamphongo zija, pa nkhosa zamphongo zija, ndi pa anaankhosa aja, malinga ndi chiŵerengero cha nyamazo ndi potsata malangizo ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pamodzi ndi ngʼombe zazimuna, nkhosa zazimuna ndi ana ankhosa, muzipereka zopereka za chakudya ndi za chakumwa molingana ndi chiwerengero cha nyamazo. Onani mutuwo |