Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 29:20 - Buku Lopatulika

20 Ndi tsiku lachitatu ng'ombe khumi ndi imodzi, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai a chaka chimodzi opanda chilema;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndi tsiku lachitatu ng'ombe khumi ndi imodzi, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai a chaka chimodzi opanda chilema;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 “Pa tsiku lachitatu mupereke ng'ombe zamphongo khumi ndi imodzi, nkhosa ziŵiri zamphongo, anaankhosa khumi ndi anai amphongo, a chaka chimodzi, opanda chilema,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 “ ‘Pa tsiku lachitatu muzipereka ngʼombe zazimuna khumi ndi imodzi, nkhosa zazimuna ziwiri ndi ana ankhosa aamuna khumi ndi anayi a chaka chimodzi, zonse zopanda chilema.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 29:20
4 Mawu Ofanana  

Ndipo tsiku lachiwiri muzibwera nazo ng'ombe zamphongo khumi ndi ziwiri, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai a chaka chimodzi, opanda chilema;


ndi tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira.


ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake;


Koma pamene padafika pakati pa chikondwerero, Yesu anakwera nalowa mu Kachisi, naphunzitsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa