Numeri 28:24 - Buku Lopatulika24 Momwemo mupereke chakudya cha nsembe yamoto cha fungo lokoma la Yehova, tsiku ndi tsiku, masiku asanu ndi awiri, chakupereka pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yothira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Momwemo mupereke chakudya cha nsembe yamoto cha fungo lokoma la Yehova, tsiku ndi tsiku, masiku asanu ndi awiri, chakupereka pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yothira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Motero pa masiku asanu ndi aŵiri muzipereka tsiku lililonse chakudya cha nsembe yotentha pa moto, yotulutsa fungo lokomera Chauta. Muchipereke kuwonjezera pa nsembe zopsereza za tsiku ndi tsiku zija pamodzi ndi zopereka za chakumwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Motere muzikonza chakudya cha nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku pa masiku asanu ndi awiri ngati fungo lokomera Yehova. Zimenezi ziziperekedwa kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya nthawi zonse pamodzi ndi nsembe yachakumwa. Onani mutuwo |