Numeri 28:23 - Buku Lopatulika23 Mupereke izi pamodzi ndi nsembe yopsereza ya m'mawa, ndiyo ya nsembe yopsereza kosalekeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Mupereke izi pamodzi ndi nsembe yopsereza ya m'mawa, ndiyo ya nsembe yopsereza kosalekeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Muzipereka zimenezi kuwonjezera pa nsembe zopsereza za tsiku ndi tsiku zopereka nthaŵi yam'maŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Muzikonza zimenezi nthawi zonse, powonjezera pa nsembe yopsereza ya mmawa. Onani mutuwo |