Numeri 26:53 - Buku Lopatulika53 Dziko ligawikire iwowa monga mwa kuwerenga kwa maina, likhale cholowa chao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Dziko ligawikire iwowa monga mwa kuwerenga kwa maina, likhale cholowa chao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 “Uŵagaŵire dziko anthu ameneŵa, kuti likhale choloŵa chao, molingana ndi chiŵerengero cha maina ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 “Uwagawire dziko anthu awa kuti likhale cholowa chawo molingana ndi chiwerengero cha mayina awo. Onani mutuwo |