Numeri 26:50 - Buku Lopatulika50 Iwo ndiwo mabanja a Nafutali, monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 Iwo ndiwo mabanja a Nafutali, monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 Ameneŵa, anthu okwanira 45,400, ndiwo adaŵerengedwa pa mabanja a Nafutali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Awa ndiwo anali mafuko a Nafutali. Onse amene anawerengedwa analipo 45,400. Onani mutuwo |