Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 26:49 - Buku Lopatulika

49 Yezere, ndiye kholo la banja la Ayezere; Silemu, ndiye kholo la banja la Asilemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

49 Yezere, ndiye kholo la banja la Ayezere; Silemu, ndiye kholo la banja la Asilemu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

49 Yezere anali kholo la banja la Ayezere. Silemu anali kholo la banja la Asilemu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

49 kuchokera mwa Yezeri, fuko la Ayezeri; kuchokera mwa Silemu, fuko la Asilemu.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:49
2 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Nafutali: Yazeele, ndi Guni, ndi Yezere ndi Silemu.


Ana a Nafutali: Yaziyele, ndi Guni, ndi Yezere, ndi Salumu, ana a Biliha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa