Numeri 26:48 - Buku Lopatulika48 Ana aamuna a Nafutali monga mwa mabanja ao ndiwo: Yazeele, ndiye kholo la banja la Ayezeele; Guni, ndiye kholo la banja la Aguni; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 Ana amuna a Nafutali monga mwa mabanja ao ndiwo: Yazeele, ndiye kholo la banja la Ayezeele; Guni, ndiye kholo la banja la Aguni; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Potsata mabanja ao ana aamuna a Nafutali anali aŵa: Yazeele anali kholo la banja la Ayazeele. Guni anali kholo la banja la Aguni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Zidzukulu za Nafutali mwa mafuko awo zinali izi: kuchokera mwa Yahazeeli, fuko la Ayahazeeli; kuchokera mwa Guni, fuko la Aguni; Onani mutuwo |