Numeri 26:47 - Buku Lopatulika47 Iwo ndiwo mabanja a ana aamuna a Asere monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Iwo ndiwo mabanja a ana amuna a Asere monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Ameneŵa, anthu okwanira 53,400, ndiwo adaŵerengedwa pa mabanja a Asere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Awa ndiwo anali mafuko a Aseri. Onse amene anawerengedwa analipo 53,400. Onani mutuwo |