Numeri 26:41 - Buku Lopatulika41 Iwo ndiwo ana a Benjamini monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Iwo ndiwo ana a Benjamini monga mwa mabanja ao; ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Ameneŵa, anthu okwanira 45,600, ndiwo anali a m'mabanja a Benjamini, amene adaŵerengedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Awa ndiwo anali mabanja a Benjamini. Amene nawerengedwa analipo 45,600. Onani mutuwo |