Numeri 26:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo ana aamuna a Bela ndiwo Aridi ndi Naamani; Aridi, ndiye kholo la banja la Aaridi; Naamani, ndiye kholo la banja la Anaamani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo ana amuna a Bela ndiwo Aridi ndi Naamani; Aridi, ndiye kholo la banja la Aaridi; Naamani, ndiye kholo la banja la Anaamani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Ndipo ana aamuna a Bela anali Aradi ndi Namani. Aradi anali kholo la banja la Aaradi. Namani anali kholo la banja la Anamani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Zidzukulu za Bela kupyolera mwa Aridi ndi Naamani zinali izi: kuchokera mwa Aridi, fuko la Aaridi; kuchokera mwa Naamani, fuko la Anaamani; Onani mutuwo |