Numeri 26:39 - Buku Lopatulika39 Sefufamu ndiye kholo la banja la Asefufamu; Hufamu, ndiye kholo la banja la Ahufamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Sefufamu ndiye kholo la banja la Asefufamu; Hufamu, ndiye kholo la banja la Ahufamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Sefufamu anali kholo la banja la Asefufamu. Hafamu anali kholo la banja la Ahufamu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 kuchokera mwa Sufamu, fuko la Asufamu; kuchokera mwa Hufamu, fuko la Ahufamu; Onani mutuwo |