Numeri 26:32 - Buku Lopatulika32 ndi Semida, ndiye kholo la banja la Asemida; ndi Hefere, ndiye kholo la banja la Ahefere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 ndi Semida, ndiye kholo la banja la Asemida; ndi Hefere, ndiye kholo la banja la Ahefere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Semida anali kholo la banja la Asemida. Hefere anali kholo la banja la Ahefere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 kuchokera mwa Semida, fuko la Asemida; kuchokera mwa Heferi, fuko la Aheferi. Onani mutuwo |