Numeri 26:31 - Buku Lopatulika31 ndi Asiriele, ndiye kholo la banja la Aasiriele; ndi Sekemu, ndiye kholo la banja la Asekemu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 ndi Asiriele, ndiye kholo la banja la Aasiriele; ndi Sekemu, ndiye kholo la banja la Asekemu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Ndipo Asiriele anali kholo la banja la Aasiriele. Sekemu anali kholo la banja la Asekemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 kuchokera mwa Asirieli, fuko la Aasirieli; kuchokera mwa Sekemu, fuko la Asekemu; Onani mutuwo |