Numeri 26:30 - Buku Lopatulika30 Ana a Giliyadi ndiwo: Iyezere, ndiye kholo la banja la Aiyezere; Heleki, ndiye kholo la banja la Aheleki; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ana a Giliyadi ndiwo: Iyezere, ndiye kholo la banja la Aiyezere; Heleki, ndiye kholo la banja la Aheleki; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Ana aamuna a Giliyadi anali aŵa: Iyezere anali kholo la banja la Aiyezere. Heleki anali kholo la banja la Aheleki. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Izi ndizo zinali zidzukulu za Giliyadi; kuchokera mwa Iyezeri, fuko la Aiyezeri; kuchokera mwa Heleki, fuko la Aheleki; Onani mutuwo |