Numeri 25:2 - Buku Lopatulika2 popeza anaitana anthuwo adze ku nsembe za milungu yao; ndipo anthuwo anadya, nagwadira milungu yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 popeza anaitana anthuwo adze ku nsembe za milungu yao; ndipo anthuwo anadya, nagwadira milungu yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Akaziwo ankaitana amuna ku nsembe za milungu yao, ndipo amunawo ankadya nawo, ndi kumapembedza milungu yaoyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 amene ankawayitana ku nsembe za milungu yawo. Anthuwo anadya chakudya chopereka kwa milungu ndi kupembedza milunguyo. Onani mutuwo |