Numeri 25:3 - Buku Lopatulika3 Pamene Israele anaphatikana ndi Baala-Peori, Yehova anapsa mtima pa Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pamene Israele anaphatikana ndi Baala-Peori, Yehova anapsa mtima pa Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Choncho Aisraele adapembedza nao Baala wa ku Peori, ndipo Chauta adaŵapsera mtima Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Motero Aisraeli anapembedza nawo Baala-Peori ndipo Yehova anawapsera mtima kwambiri. Onani mutuwo |