Numeri 25:12 - Buku Lopatulika12 Chifukwa chake nena, Taonani, ndimpatsa iye pangano langa la mtendere; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Chifukwa chake nena, Taonani, ndimpatsa iye pangano langa la mtendere; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Motero umuuze kuti ndikupangana naye tsopano chipangano chamtendere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Tsono muwuze kuti ndikhazikitsa pangano langa la mtendere ndi iye. Onani mutuwo |