Numeri 24:24 - Buku Lopatulika24 Koma zombo zidzafika kuchokera ku dooko la Kitimu, ndipo adzasautsa Asiriya, nadzasautsa Eberi, koma iyenso adzaonongeka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Koma zombo zidzafika kuchokera ku dooko la Kitimu, ndipo adzasautsa Asiriya, nadzasautsa Eberi, koma iyenso adzaonongeka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Zombo zidzabwera kuchokera ku Kitimu, zidzaononga Asuri ndi Eberi. Kitimu nayenso adzaonongeka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Sitima zapamadzi zidzabwera kuchokera ku madooko a Kitimu; kupondereza Asuri ndi Eberi, koma iwonso adzawonongeka.” Onani mutuwo |