Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 24:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ha! Adzakhala ndi moyo ndani pakuchita ichi Mulungu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ha! Adzakhala ndi moyo ndani pakuchita ichi Mulungu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Adayamba kulankhulanso nati, “Kalanga ine, ndani akhale moyo, Mulungu akachita zimenezi?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Ndipo ananenanso uthenga wina kuti, “Aa, ndani adzakhala ndi moyo Mulungu akachita zimenezi?

Onani mutuwo Koperani




Numeri 24:23
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Naamani kazembe wa khamu la nkhondo la mfumu ya Aramu anali munthu womveka pamaso pa mbuyake, ndi waulemu; popeza mwa iye Yehova adapulumutsa Aaramu; ndiyenso ngwazi, koma wakhate.


Koma ndani adzapirira tsiku la kudza kwake? Ndipo adzaima ndani pooneka Iye? Pakuti adzanga moto wa woyenga, ndi sopo wa otsuka;


Pakuti palibe nyanga pakati pa Yakobo, kapena ula mwa Israele; pa nyengo yake adzanena kwa Yakobo ndi Israele, chimene Mulungu achita.


Koma Kaini adzaonongeka, kufikira Asiriya adzakumanga nsinga.


Koma zombo zidzafika kuchokera ku dooko la Kitimu, ndipo adzasautsa Asiriya, nadzasautsa Eberi, koma iyenso adzaonongeka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa