Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 24:22 - Buku Lopatulika

22 Koma Kaini adzaonongeka, kufikira Asiriya adzakumanga nsinga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Koma Kaini adzaonongeka, kufikira Asiriya adzakumanga nsinga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 komabe mudzaonongeka inu ana a Kaini, mudzakhala mu ukapolo wa Asuri nthaŵi yaitali.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 komabe inu Akeni mudzawonongedwa, pamene Asuri adzakutengeni ukapolo.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 24:22
8 Mawu Ofanana  

M'dziko momwemo iye anatuluka kunka ku Asiriya, namanga Ninive, ndi mzinda wa Rehoboti, ndi Kala,


Ndiponso kwa Semu atate wa ana onse a Eberi, mkulu wa Yafeti, kwa iye kunabadwa ana.


Ana aamuna a Semu; Elamu, ndi Asiriya, ndi Aripakisadi, ndi Ludi, ndi Aramu.


Akeni ndi Akenizi, Akadimoni,


anayandikira kwa Zerubabele, ndi kwa akulu a nyumba za makolo, nanena nao, Timange pamodzi nanu; pakuti timfuna Mulungu wanu monga inu, ndipo timamphera nsembe chiyambire masiku a Esarahadoni mfumu ya Asiriya, amene anatikweretsa kuno.


Asiriya anaphatikana nao; anakhala dzanja la ana a Loti.


Asiriya sadzatipulumutsa; sitidzayenda pa akavalo, ndipo sitidzanenanso kwa ntchito ya manja athu, Inu ndinu milungu yathu; pakuti mwa Inu ana amasiye apeza chifundo.


Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ha! Adzakhala ndi moyo ndani pakuchita ichi Mulungu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa