Numeri 24:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anayang'ana Akeni, nanena fanizo lake, nati, kwanu nkokhazikika, wamanga chisa chako m'thanthwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anayang'ana Akeni, nanena fanizo lake, nati, kwanu nkokhazikika, wamanga chisa chako m'thanthwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Kenaka adayang'ana Akeni, tsono adayamba kulankhula nati, “Ngakhale malo amene mukukhalawo ngopanda zovuta, monga chisa chomangidwa pa thanthwe, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kenaka anaonanso Akeni ndipo ananena uthenga wake, “Malo amene mukukhalamo ndi otetezedwa, chisa chanu chinayikidwa pa thanthwe; Onani mutuwo |