Numeri 24:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo anayang'ana ku Amaleke, nanena fanizo lake, nati, Amaleke ndiye woyamba wa amitundu; koma chitsiriziro chake, adzaonongeka ku nthawi zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo anayang'ana ku Amaleke, nanena fanizo lake, nati, Amaleke ndiye woyamba wa amitundu; koma chitsiriziro chake, adzaonongeka ku nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsono Balamu adayang'ana Amaleke, ndipo adayamba kulankhula nati, “Mtundu wa Amaleke udaali wopambana mitundu ina yonse, koma potsiriza pake udzaonongeka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Kenaka Balaamu anaona Aamaleki ndipo ananena uthenga wake uwu: “Aamaleki anali oyamba mwa mitundu ya anthu koma potsiriza pake adzawonongeka.” Onani mutuwo |