Numeri 24:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo wina wotuluka mu Yakobo adzachita ufumu; nadzapasula otsalira m'mizinda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo wina wotuluka m'Yakobo adzachita ufumu; nadzapasula otsalira m'mudzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Mwa Yakobe mudzatuluka mfumu yolamulira, imene idzaononga otsala mu mzinda.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Wolamulira adzachokera mwa Yakobo ndipo adzawononga otsala a mu mzindamo.” Onani mutuwo |