Numeri 24:18 - Buku Lopatulika18 Ndi Edomu adzakhala akeake, Seiri lomwe lidzakhala lakelake, ndiwo adani ake; koma Israele adzachita zamphamvu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndi Edomu adzakhala akeake, Seiri lomwe lidzakhala lakelake, ndiwo adani ake; koma Israele adzachita zamphamvu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Dziko la Edomu lidzalandidwa, Seiri mdani wake adzagonjetsedwa, pamene Aisraele adzakhala akupambanabe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Edomu adzagonjetsedwa; Seiri, mdani wake, adzawonongedwa koma mphamvu za Israeli zidzachuluka. Onani mutuwo |