Numeri 23:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Balaki anati kwa Balamu, Usawatemberera konse, kapena kuwadalitsa konse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Balaki anati kwa Balamu, Usawatemberera konse, kapena kuwadalitsa konse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Balaki adauza Balamu kuti, “Musaŵatemberere, ndipo musaŵadalitse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ndipo Balaki anati kwa Balaamu, “Usawatemberere ndi pangʼono pomwe kapena kuwadalitsa! Onani mutuwo |