Numeri 23:24 - Buku Lopatulika24 Taonani, anthuwo auka ngati mkango waukazi, nadzitukumula ngati mkango waumuna. Sugonanso kufikira utadya nyama yogwira, utamwa mwazi wa zophedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Taonani, anthuwo auka ngati mkango waukazi, nadzitukumula ngati mkango waumuna. Sugonanso kufikira utadya nyama yogwira, utamwa mwazi wa zophedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Onani Aisraele, kudzuka kwanu kuli ngati kwa mkango waukazi, kudzambatuka kwanu kuli ngati kwa mkango waumuna, umene sugona pansi mpaka utagwira nyama ndi kuidya ndi kumwa magazi ake a nyama yojiwayo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Taonani, anthu anyamuka ngati mkango waukazi; adzuka okha ngati mkango waumuna umene supuma mpaka utadya nyama imene wagwira ndi kumwa magazi a nyama yogwidwayo.” Onani mutuwo |