Numeri 23:21 - Buku Lopatulika21 Sayang'anira mphulupulu ili mu Yakobo, kapena sapenya kupulukira kuli mu Israele. Yehova Mulungu wake ali ndi iye, ndi mfuu wa mfumu uli pakati pao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Sayang'anira mphulupulu ili m'Yakobo, kapena sapenya kupulukira kuli m'Israele. Yehova Mulungu wake ali ndi iye, ndi mfuu wa mfumu uli pakati pao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Iye sadaone choipa mwa Yakobe, sadaone chovuta mwa Israele. Chauta wao ali nawo, ndipo pakati pao pali kufuula kuti Iye ndi mfumu yao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 “Palibe kuwukira kulikonse kumene wakuona mwa Yakobo, sanaone chovuta mu Israeli. Yehova Mulungu wawo ali nawo: mfuwu wa mfumu uli pakati pawo. Onani mutuwo |