Numeri 23:22 - Buku Lopatulika22 Mulungu awatulutsa mu Ejipito; mphamvu yake ikunga ya njati. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Mulungu awatulutsa m'Ejipito; mphamvu yake ikunga ya njati. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Mulungu adaŵatulutsa m'dziko la Ejipito, ali ndi mphamvu zonga za njati. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Mulungu wowatulutsa mʼdziko la Igupto, ali ndi mphamvu ngati za njati. Onani mutuwo |