Numeri 23:20 - Buku Lopatulika20 Kapena kulankhula, osachitsimikiza? Taonani, ndalandira mau akudalitsa, popeza Iye wadalitsa, sinditha kusintha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Kapena kulankhula, osachitsimikiza? Taonani, ndalandira mau akudalitsa, popeza Iye wadalitsa, sinditha kusintha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ndithu, ndalandira lamulo kuti ndidalitse. Iye wadalitsa, ndipo ine sindingathe kusintha kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Wandilamula kuti ndidalitse, Iyeyo wadalitsa ndipo sindingasinthe. Onani mutuwo |