Numeri 23:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Yehova anakomana naye Balamu, naika mau m'kamwa mwake, nati, Bwerera kwa Balaki, nukanene chakutichakuti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Yehova anakomana naye Balamu, naika mau m'kamwa mwake, nati, Bwerera kwa Balaki, nukanene chakutichakuti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Chauta adakumana naye Balamu namuuza kuti, “Bwerera kwa Balaki, ndipo umuuze izi! Izi!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Yehova anakumana ndi Balaamu ndipo anamuyankhula kuti, “Bwerera kwa Balaki ndipo ukamuwuze uthenga uwu.” Onani mutuwo |