Numeri 22:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo Balamu anamuka ndi Balaki, nafika iwo ku Kiriyati-Huzoti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo Balamu anamuka ndi Balaki, nafika iwo ku Kiriyati-Huzoti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Tsono Balamu adapita limodzi ndi Balaki, nakafika ku Kiriyati-Huzoti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Pamenepo Balaamu anapita pamodzi ndi Balaki ku Kiriati-Huzoti. Onani mutuwo |