Numeri 22:40 - Buku Lopatulika40 Pamenepo Balaki anapha ng'ombe ndi nkhosa, natumizira Balamu, ndi akalonga okhala naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Pamenepo Balaki anapha ng'ombe ndi nkhosa, natumizira Balamu, ndi akalonga okhala naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Kumeneko Balaki adapereka nsembe ya ng'ombe ndi nkhosa, natumizako nyama kwa Balamu ndi kwa akalonga amene anali naye aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Balaki anapereka nsembe ngʼombe ndi nkhosa, ndipo anapereka zina kwa Balaamu ndi kwa akuluakulu omwe anali naye. Onani mutuwo |