Numeri 22:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Taonani, ndafika kwa inu; ngati ndili nayo mphamvu konse tsopano kunena kanthu? Mau amene Mulungu aike m'kamwa mwanga ndiwo ndidzanena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Taonani, ndafika kwa inu; ngati ndili nayo mphamvu konse tsopano kunena kanthu? Mau amene Mulungu aike m'kamwa mwanga ndiwo ndidzanena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Balamu adayankha Balaki kuti, “Inde, ndabwera, koma kodi ndili ndi mphamvu zoti ndilankhule chinthu chilichonse? Ndiyenera kulankhula zokhazo zimene Mulungu andiwuze.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Balaamu anayankha Balaki kuti, “Taonani, ndabwera kwa inu lero, kodi ine ndili ndi mphamvu zoti nʼkuyankhula chilichonse? Inetu ndiyenera kuyankhula zokhazo zimene Mulungu wandiwuza.” Onani mutuwo |