Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 22:26 - Buku Lopatulika

26 Pamenepo mthenga wa Yehova anapitiriranso, naima popapatiza, popanda popatukira kulamanja kapena kulamanzere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Pamenepo mthenga wa Yehova anapitiriranso, naima popapatiza, popanda popatukira kulamanja kapena kulamanzere.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Kenaka mngelo wa Chauta adatsogolako nakaimiriranso pa malo ophaphatiza, opanda koti nkutembenukira kumanja kapena kumanzere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Kenaka mngelo wa Yehova anapita patsogolo ndi kuyima pamalo opanikizika pomwe panalibe poti nʼkutembenukira ku dzanja lamanja kapena lamanzere.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 22:26
4 Mawu Ofanana  

Yehova, dzanja lanu litukulidwa, koma iwo saona; koma iwo adzaona changu chanu cha kwa anthu, nadzakhala ndi manyazi; inde moto udzamaliza adani anu.


Chifukwa chake taonani, ndidzatchinga njira yako ndi minga, ndipo ndidzammangira mpanda, kuti asapeze mabande ake.


Ndipo bulu anaona mthenga wa Yehova, nadzikankhira kulinga, nakanikiza phazi la Balamu kulinga; ndipo anampandanso.


Ndipo bulu wake anaona mthenga wa Yehova, nagona pansi, Balamu ali pamsana pake; ndipo Balamu adapsa mtima, nampanda bulu ndi ndodo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa