Numeri 22:24 - Buku Lopatulika24 Pamenepo mthenga wa Yehova anaima m'njira yopapatiza ya minda yampesa; mbali ina kuli linga, mbali ina linga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Pamenepo mthenga wa Yehova anaima m'njira yopapatiza ya minda yampesa; mbali ina kuli linga, mbali ina linga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Pambuyo pake mngelo wa Chauta uja adakaimirira m'kanjira kophaphatiza, kodzera pakati pa minda yamphesa, kokhala ndi khoma pa mbali zonse ziŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Kenaka mngelo wa Yehova anayima mʼkanjira kakangʼono pakati pa minda iwiri ya mpesa yokhala ndi makoma mbali zonse Onani mutuwo |