Numeri 22:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo buluyo anaona mthenga wa Yehova alikuima m'njira, ndi lupanga lake ku dzanja lake; ndi bulu anapatuka m'njira, nalowa kuthengo; ndipo Balamu anampanda bulu kumbwezera kunjira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo buluyo anaona mthenga wa Yehova alikuima m'njira, ndi lupanga lake ku dzanja lake; ndi bulu anapatuka m'njira, nalowa kuthengo; ndipo Balamu anampanda bulu kumbwezera kunjira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Bulu uja adaona mngelo wa Chauta ataima mu mseu, atasolola lupanga m'manja mwake. Tsono bulu adasiya mseu nakaloŵa m'munda. Apo Balamu adammenya bulu uja kuti abwerere mu mseu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pamene buluyo anaona mngelo wa Yehova atayima pa njira ndi lupanga mʼmanja mwake, anapatukira kumbali kwa msewu napita kutchire. Balaamu anamumenya kuti abwerere mu msewu. Onani mutuwo |